Pena timatha kukhomereledwa zintchito ndi ma bwana olo azizanthu omwewa kamba kokuti tinazolowela mavuto.
Koma poti ndife anthu alimbika timafunabe moyo wosangala always.
Tanvelani nyimboyi ikufotokoza zambiri za lifestyle yomwe timafuna.
- Producer:Bispa on the bord
- Release Date:December 15, 2024



