|
|
Upload
Real Nikka by Nospee NN'OI
Real Nikka by Nospee NN'OI

Nospee NN'OIReal Nikka

Nospee NN'OIReal Nikka

0:00
0.00% played
0:00

Uploaded By

VIEW PROFILE
Avatar

421 Followers

Real Nikka Verse I Ndili mkati yeah nikka nde ndufila real Sungathayime pano ndikupanga zina Khethana mafana tikukhethanabe Shit yi ndiyi koma tikuthoka ndife Sangawone komwe tikuthayimila nduko👉🏾 Mix timakhala kuti tili mtika Broh shit ndiyi ife tili real Sitingakunamize iwe no chill Tingo KNØK apa ndiye tikupita Sangaziwe pomwe tikulowela ndi Share Hook fact timathoka ife timakakha fact timathoka ife timakakha Verse II Mesa ndimatchula ngati ndikuyima (fact) Mesa ndango trod ah ine ndikupita (fact) Ona ndimaso anga iwe uku trod ah(fact) Mesa uku trapper sxit sukuwona Wa blind wangowona ekha sawona Mesa mission imatheka ndeno tawona Maso anga SI a khungu ndayamba kuwona Zamudima zonse ndazidziwa nditawona Nkhani zija ulemu wake ndazitolela Ndimafuna kuti maso anga atatseguka Shit ndimathoka ndikudziwa ndimawona Kukola ngati spiderman ndilino pakhoma Singanene zawo chifukwa anamagona Akuthoka ngini yoti sakuyitolela Samathoka ndani? poti ife timawona Tasiyila zonse manja mwawo akuwona Game inawakulila koma amagona Samaziwa kuti alowela powawona Shit Ndiya bho bola akuyitila Samaziwa kt zikhala ngati mbwelela. Voice + Beat produced by Nospee NN'OI
  • Release Date:November 11, 2026
  • Producer:Nospee NN'OI
  • Genre:Hip-Hop/Rap
36Total plays
4Likes
1Re-Ups