Uploaded By
VIEW PROFILE
3.71K Followers
Urban Link Musical Village
Verse - Mic Mash
Amadyetsa mbalame zosalima
Amalimbitsa zonse zosakhwima
Moyo waulele anandipatsa ambiri ma hour
Ndilibe chifukwa chodandaulaso za mawa
Mavuto angalimbe, Hakuna Matata, I matter to my father andisamala
Dziko lingandinyoze, sindichita mantha, I’m never alone// I’ll never worship other gods like Aaron
Sawelengela phulupulu zanga
Zomwe ndimachita ndi anzanga
Ngakhale ndimachimwa mbuye wanga sanditaya
Ine ndikamaphwa iye amandipopa ngati tire
(Eeeeh Eeeh) you gave me life I lift your name higher
(Eeeh eeeh) you the reason why ndikuimba ndi choir
Ndithange ufumu wanu zinthu zanu ndizakwaya
At the end of the day I don’t want to go to fire
Hook - Siggy Kim
Andisamala andisamala
Andisamala amasamala adzasamala
Andisamala andisamala
Andisamala amasamala adzasamala
Andisamala andisamala
Andisamala amasamala adzasamala
Verse 2- Siggy Kim
Feedi
- Release Date:December 17, 2018Ⓡ
- Album:Mirror LP
- Producer:SevenOmore & Manifest
- Genre:Hip-Hop/Rap







0 comments