Tatiyeni tinvere chinyimbo cha bwno chokoma🔥🔥🔥🔥
Anati azabwela kuzamuona mwana zikazayenda ku joni ko komano sabwela mpaka zaka zikutha mwana akukula popanda chikondi cha bambo ake. Amuna ambili makwalalamu anachoka nkunena kuti akukasaka nchto kusiya mkadzi ndi ana komano samabwelela uthengawu ndi wanu mubwele komwe muliko makomomu muli mavuto osyana syana...
- Release Date:November 22, 2025
- Album:single

![Mubwele[prod.by Randetta] by Lady Snazzy](https://i.audiomack.com/ladysnazzy118/2f8f265a50.webp?width=360)