Mkazi Ndiwofatsa Ndiwakuda Ndiwa Shape Ngati Zani Chale /Kamafila Nyimbo Zaku Malawi/ Artist Yemwe Amafira Ndi Lawi /Ndakatalker Nane Ndine Mfana Wapakathawi! /Ndimafila "LuLu"! Kandinong'oneza Ku Khuku She Said /Kati Yeyo Ndine Mpaka Lululu/To Be Honest I Jus wanna be Wit You /Tingothawitsa! Tingopita Ku Mpoto Sumapanga Nawo Zo Trippa........
- Producer:Izes Khalida
- Release Date:January 29, 2025
- Album:Single




