Uploaded By
VIEW PROFILE
4.77K Followers
Lyrics
Intro💥
Sanje ' Sanje
Mmmmm ' Sanje Sanje
Verse1💥
Mtima mwanga mwangodzadza 'Sanje'×2
Nanji ndikakuona ndiwina ine Sanjeeee
Ndimadzifusa kodi ndikhala bwanji
Mtima mwanga mwangodzadza 'Sanje'×2
Zoti unagwidwa ndi wina ine sanje
Aaa ine sanjeeeaaaie
Bridge💥
Nanji nkakuona pa status
Yah ukuti ndani Your new boyfriend Yeah
Nanji nkakuona pa status
My heartbeat increase
Hook💥
Sanje' Sanje
Mmmm aaa Sanje' Sanje
Mmmmmmm Ndangodzadziwaaaaa
Sanje' Sanjeeeee Ndangodzadzidwaaaaa
Sanje' Sanje mmmmm ndangodzadzidwaaaa
Verse💥
Ndayesera kupilira Mmmmmm
Ndayesera Kuiwala
Koma mumtima mwanga sukuchoka mmm
Mwina nkumati ndi tsoka
'Chifukwa yandivuta'
Hook💥👆
Repeat Verse1 then Bridge n Hook...
@FireRecordsMalawi
- Release Date:September 12, 2023Ⓡ
- Album:Jealousy Album
- Producer:Fir Record
- Genre:Afrosounds





0 comments