Lyrics 👇
Intro
(karate sounds)
Mmmmmmm yeeieeea
Verse 1
Okufuna nzamuonetsa "Karate"×3
Zaiwe wekha ndikafika "pa court"×3
Nzakukonda nthawi zonse "no chuthi"×2
Uli fire ngati mfuti
Okufuna nzamuponda ndi buti "ndi buti"
No mistake ndizachepetsa "ma fault"×3
Iwe ndinawina ngati "mavoti"×3
Kukuvetsa koma ngati "ma fruit"×3
So lets never fell "apart"×3
Chorus
Ndeno...
- Producer:Fir Record
- Release Date:September 23, 2023Ⓡ
- Album:Karate_Ep





