Download it in the appChikondi, chikondi ndichowawa
Ndichowawa Chikondi
Chikondi chokakamilana//
Sakufuna kukhala nawe, Sakhutistidwa ndi mmodzi
Chifukwa anapeza money, muumphawi munali limodzi
Analumbila pa guwa, muzakalambila limodzi
Pano sakufuna, ukugwetsa misoxi//
Chikondi, chikondi ndichowawa
Ndichowawa Chikondi
Chikondi chokakamilana//
Verse
Kulusa ukagwira phone, amaziwa muli ngini
Kuchedwa kupanda respond, dziwa mulipo awiri
Nzakoyotu ndikatswiri, Ati akupanga mbiri
Nkhope yake ndiyofatsa koma Mtima wake ndi wa mphiri
Anzanu aja ndichinjoka,...
- Producer:Shilton Kankhuni
- Release Date:October 13, 2023
- Album:WET BRAINS - [Tape 1]