|
|
Upload
Ndizova by Crispy Malawi & Dirty flo
Ndizova by Crispy Malawi & Dirty flo

Crispy Malawi & Dirty floNdizova

Crispy Malawi & Dirty floNdizova

0:00
0.00% played
0:00

Uploaded By

VIEW PROFILE
Avatar

97.7K Followers

Dirty Flo & Crispy Malawi - Ndizovaya (Intro) “Ngati Sumafila Zomwe ndimapanga ingotseka Maso “ x 2 Ma Lawyer Ama Judger Nyimbo zathu Ma Nurse sangachize flow yathu Ma Blessings amazela njira Yathu Ma Rasta Amafeela Chamba Chathu Ndizovaya (yeah) x8 (Verse 1 ) Ngati Sumafila zomwe ndipanga jngoseka Maso Line Yaku Show Ngati Fans Ikusaka Gaso Ku chi Corner Ngati mwina Ndimaimba Dancehall Nyimbo zavaya Kale kunja koma opanda passport Akuuzani kuti anawo ndi smoko ndi blanda Boys ili boys quarter kumvela boys siizamva Akatispotta kuluza control they go wild ah iwe Amatiwelengela taapolesa ku library yeah Ndikufuna One On One Meeting ndi Major (one) Ndiboys tikuyenda mma College Zau Lecture Ati ndikusowa koma Pa Google akumandipeza Ma Punchiline onsewa ndizosatheka
  • Release Date:January 13, 2023
  • Album:RNB
  • Producer:Wylie Famous Chilunga
  • Genre:Hip-Hop/Rap
15.8KTotal plays
79Likes
6Re-Ups
109Playlist Adds

Playlists Featuring Artist

0 comments