Uploaded By
VIEW PROFILE
6 Followers
Usiku Omaliza omwe bambo anasanzika Banjala kale kupita kogwila ntchito, koma omwewo osazabwelanso. Mayi atatopa ndikusamala ana yekha sakanachitila mwina koma nayeso ukuwona nsana wanjila, mkusiya ana okhaokha tikunena pano anawo alipamavuto azawoneni.
- Release Date:April 16, 2023
- Album:YIWE!!!!!
- Producer:DJ Nusko x Bispar
- Genre:Afrosounds






0 comments